Yeremiya 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘“Mzinda uwu ndaukana* ndipo ukumana ndi tsoka osati zabwino,”+ watero Yehova. “Ndidzaupereka m’manja mwa mfumu ya Babulo+ ndipo idzautentha ndi moto.”+ Yeremiya 32:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Yehova wanena kuti, ‘Tsopano ndikupereka mzinda uwu m’manja mwa Akasidi ndi m’manja mwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo, ndipo aulanda.+
10 “‘“Mzinda uwu ndaukana* ndipo ukumana ndi tsoka osati zabwino,”+ watero Yehova. “Ndidzaupereka m’manja mwa mfumu ya Babulo+ ndipo idzautentha ndi moto.”+
28 Choncho Yehova wanena kuti, ‘Tsopano ndikupereka mzinda uwu m’manja mwa Akasidi ndi m’manja mwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo, ndipo aulanda.+