Ezekieli 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, “Pali ine Mulungu wamoyo,+ munthu amene ananyoza lumbiro+ ndi kuphwanya pangano limene anachita ndi mfumu imene inamulonga ufumu, adzafera m’dziko la mfumu yomweyo, dziko la Babulo.+
16 “‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, “Pali ine Mulungu wamoyo,+ munthu amene ananyoza lumbiro+ ndi kuphwanya pangano limene anachita ndi mfumu imene inamulonga ufumu, adzafera m’dziko la mfumu yomweyo, dziko la Babulo.+