Yeremiya 37:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno gulu lankhondo la Farao linabwera kuchokera ku Iguputo.+ Akasidi amene anali atazungulira mzinda wa Yerusalemu atamva zimenezi anachoka ku Yerusalemu.+
5 Ndiyeno gulu lankhondo la Farao linabwera kuchokera ku Iguputo.+ Akasidi amene anali atazungulira mzinda wa Yerusalemu atamva zimenezi anachoka ku Yerusalemu.+