15 Koma iye anapandukira+ mfumuyo potumiza amithenga ku Iguputo kuti dziko la Iguputo limupatse mahatchi+ ndi khamu la anthu. Kodi zinthu zidzamuyendera bwino? Kodi munthu amene akuchita zinthu zimenezi ndiponso amene akuphwanya pangano adzapulumuka? Kodi iye adzapulumukadi?’+