2 Mafumu 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kuwonjezera apo, Farao Neko anaika Eliyakimu+ mwana wa Yosiya kukhala mfumu m’malo mwa Yosiya bambo ake, n’kumusintha dzina kuti akhale Yehoyakimu. Atatero anatenga Yehoahazi n’kupita naye ku Iguputo, kumene anakafa pamapeto pake.+ 2 Mbiri 36:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehoyakimu+ anali ndi zaka 25 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wake.+ Danieli 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 M’chaka chachitatu cha ufumu wa Yehoyakimu+ mfumu ya Yuda, Nebukadinezara mfumu ya Babulo anabwera ku Yerusalemu ndipo anazungulira mzindawo.+
34 Kuwonjezera apo, Farao Neko anaika Eliyakimu+ mwana wa Yosiya kukhala mfumu m’malo mwa Yosiya bambo ake, n’kumusintha dzina kuti akhale Yehoyakimu. Atatero anatenga Yehoahazi n’kupita naye ku Iguputo, kumene anakafa pamapeto pake.+
5 Yehoyakimu+ anali ndi zaka 25 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wake.+
1 M’chaka chachitatu cha ufumu wa Yehoyakimu+ mfumu ya Yuda, Nebukadinezara mfumu ya Babulo anabwera ku Yerusalemu ndipo anazungulira mzindawo.+