2 Mafumu 23:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Yehoyakimu anali ndi zaka 25+ pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Ruma, ndipo dzina lawo linali Zebida mwana wa Pedaya. Yeremiya 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Awa ndi mawu amene Yeremiya anauzidwa onena za anthu onse a mu Yuda m’chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, chimenenso chinali chaka choyamba cha ulamuliro wa Nebukadirezara mfumu ya Babulo.
36 Yehoyakimu anali ndi zaka 25+ pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Ruma, ndipo dzina lawo linali Zebida mwana wa Pedaya.
25 Awa ndi mawu amene Yeremiya anauzidwa onena za anthu onse a mu Yuda m’chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, chimenenso chinali chaka choyamba cha ulamuliro wa Nebukadirezara mfumu ya Babulo.