Yeremiya 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako akalonga a Yuda anamva mawu amenewa ndipo anakwezeka kuchokera kunyumba ya mfumu kupita kunyumba ya Yehova.+ Kumeneko anakhala pansi pachipata chatsopano cha nyumba ya Yehova.+
10 Kenako akalonga a Yuda anamva mawu amenewa ndipo anakwezeka kuchokera kunyumba ya mfumu kupita kunyumba ya Yehova.+ Kumeneko anakhala pansi pachipata chatsopano cha nyumba ya Yehova.+