Yeremiya 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anauza Yeremiya mawu,+ pamene Mfumu Zedekiya+ inatumiza Pasuri+ mwana wa Malikiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, ndi uthenga wakuti:
21 Yehova anauza Yeremiya mawu,+ pamene Mfumu Zedekiya+ inatumiza Pasuri+ mwana wa Malikiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, ndi uthenga wakuti: