1 Samueli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Eli anamuuza kuti: “Kodi Mulungu wakuuza chiyani? Chonde usandibisire ayi.+ Mulungu akulange ndi kuwonjezerapo,+ ukandibisira ngakhale mawu amodzi pa mawu onse amene iye wakuuza.” 1 Mafumu 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno mfumuyo inamuuza kuti: “Kodi ndikulumbiritse kangati kuti uzilankhula kwa ine zoona zokhazokha m’dzina la Yehova?”+
17 Ndiyeno Eli anamuuza kuti: “Kodi Mulungu wakuuza chiyani? Chonde usandibisire ayi.+ Mulungu akulange ndi kuwonjezerapo,+ ukandibisira ngakhale mawu amodzi pa mawu onse amene iye wakuuza.”
16 Ndiyeno mfumuyo inamuuza kuti: “Kodi ndikulumbiritse kangati kuti uzilankhula kwa ine zoona zokhazokha m’dzina la Yehova?”+