Yeremiya 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ndidzakulanditsa m’manja mwa anthu oipa+ ndipo ndidzakuwombola m’manja mwa anthu ankhanza.” Yeremiya 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Ahikamu,+ mwana wa Safani+ anali kuteteza Yeremiya kuti anthu asamuphe.+