Salimo 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Khulupirira Yehova ndipo chita zabwino.+Khala padziko lapansi, ndipo khala wokhulupirika m’zochita zako zonse.+ Yeremiya 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘“‘Mtundu wa anthu umene udzaika khosi lake m’goli la mfumu ya Babulo ndi kuitumikira, ndidzauchititsa kukhala mwamtendere m’dziko lawo, ndipo adzalima minda ndi kukhalabe m’dzikomo,’ watero Yehova.”’”+
3 Khulupirira Yehova ndipo chita zabwino.+Khala padziko lapansi, ndipo khala wokhulupirika m’zochita zako zonse.+
11 “‘“‘Mtundu wa anthu umene udzaika khosi lake m’goli la mfumu ya Babulo ndi kuitumikira, ndidzauchititsa kukhala mwamtendere m’dziko lawo, ndipo adzalima minda ndi kukhalabe m’dzikomo,’ watero Yehova.”’”+