Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 38:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Yehova wanena kuti, ‘Amene adzapitirize kukhala mumzinda uno adzafa ndi lupanga,+ njala yaikulu+ kapena mliri.+ Koma amene adzadzipereke kwa Akasidi adzakhala ndi moyo. Adzapulumutsa moyo wake, sadzafa ayi.’+

  • Yeremiya 40:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani+ analumbira+ pamaso pa akuluakuluwo ndi asilikali awo kuti: “Musaope kutumikira Akasidi. Pitirizani kukhala m’dzikoli n’kumatumikira mfumu ya Babulo ndipo zinthu zikuyenderani bwino.+

  • Yeremiya 42:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 ‘Ngati mungakhalebe m’dziko lino,+ ndidzakulimbitsani osati kukupasulani, ndidzakubzalani osati kukuzulani,+ pakuti ndidzakumverani chisoni chifukwa cha tsoka limene ndakugwetserani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena