1 Samueli 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho Yonatani analumbiranso kwa Davide chifukwa chakuti anali kum’konda kwambiri. Pakuti Yonatani anali kukonda Davide monga mmene anali kudzikondera iye mwini.+ 2 Mafumu 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Gedaliya analumbirira+ akuluakuluwo ndi asilikali awo kuti: “Musaope kukhala atumiki a Akasidi. Khalani m’dzikoli n’kumatumikira mfumu ya Babulo, ndipo zinthu zikuyenderani bwino.”+
17 Choncho Yonatani analumbiranso kwa Davide chifukwa chakuti anali kum’konda kwambiri. Pakuti Yonatani anali kukonda Davide monga mmene anali kudzikondera iye mwini.+
24 Gedaliya analumbirira+ akuluakuluwo ndi asilikali awo kuti: “Musaope kukhala atumiki a Akasidi. Khalani m’dzikoli n’kumatumikira mfumu ya Babulo, ndipo zinthu zikuyenderani bwino.”+