Yeremiya 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zedekiya+ mfumu ya Yuda ndinamuuza mawu onsewa+ kuti: “Ikani makosi anu m’goli la mfumu ya Babulo ndi kuitumikira. Mutumikire mfumuyo ndi anthu ake, kuti mukhalebe ndi moyo.+ Yeremiya 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani+ analumbira+ pamaso pa akuluakuluwo ndi asilikali awo kuti: “Musaope kutumikira Akasidi. Pitirizani kukhala m’dzikoli n’kumatumikira mfumu ya Babulo ndipo zinthu zikuyenderani bwino.+
12 Zedekiya+ mfumu ya Yuda ndinamuuza mawu onsewa+ kuti: “Ikani makosi anu m’goli la mfumu ya Babulo ndi kuitumikira. Mutumikire mfumuyo ndi anthu ake, kuti mukhalebe ndi moyo.+
9 Gedaliya+ mwana wa Ahikamu+ mwana wa Safani+ analumbira+ pamaso pa akuluakuluwo ndi asilikali awo kuti: “Musaope kutumikira Akasidi. Pitirizani kukhala m’dzikoli n’kumatumikira mfumu ya Babulo ndipo zinthu zikuyenderani bwino.+