2 Mafumu 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Amoni anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova, monga anachitira Manase bambo ake.+ 2 Mafumu 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova, mogwirizana ndi zonse zimene bambo ake anachita.+