Numeri 32:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inunso mukukhala kam’badwo ka anthu ochita zoipa mofanana ndi makolo anu, kuti muwonjezere mkwiyo woyaka moto wa Yehova+ pa Isiraeli. 2 Mbiri 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ monga anachitira Manase bambo ake.+ Amoni anali kupereka nsembe+ kwa zifaniziro zonse zogoba+ zimene bambo ake+ anapanga, ndipo anapitiriza kuzitumikira.+ Machitidwe 7:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+
14 Inunso mukukhala kam’badwo ka anthu ochita zoipa mofanana ndi makolo anu, kuti muwonjezere mkwiyo woyaka moto wa Yehova+ pa Isiraeli.
22 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ monga anachitira Manase bambo ake.+ Amoni anali kupereka nsembe+ kwa zifaniziro zonse zogoba+ zimene bambo ake+ anapanga, ndipo anapitiriza kuzitumikira.+
51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+