Deuteronomo 1:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Nthawi yonseyi Yehova anali kumvetsera mawu anu. Motero anakwiya kwambiri, ndipo analumbira+ kuti, Machitidwe 7:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+
34 “Nthawi yonseyi Yehova anali kumvetsera mawu anu. Motero anakwiya kwambiri, ndipo analumbira+ kuti,
51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+