2 Mafumu 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Amoni anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova, monga anachitira Manase bambo ake.+ 2 Mbiri 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonyansa+ za mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.+ Ezekieli 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho ndinauza ana awo m’chipululu kuti,+ ‘Musayende motsatira malamulo a makolo anu,+ ndipo musasunge zigamulo zawo.+ Musadziipitse ndi mafano awo onyansa.+
2 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonyansa+ za mitundu imene Yehova anaithamangitsa pamaso pa ana a Isiraeli.+
18 Choncho ndinauza ana awo m’chipululu kuti,+ ‘Musayende motsatira malamulo a makolo anu,+ ndipo musasunge zigamulo zawo.+ Musadziipitse ndi mafano awo onyansa.+