2 Mafumu 17:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mitundu imeneyi inali kuopa Yehova,+ koma inali kutumikira zifaniziro zawo zogoba. Mpaka lero, ana awo ndi zidzukulu zawo akuchitabe mmene makolo awo ankachitira. Yesaya 44:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma mtengo wotsalawo wapangira mulungu, wapangira chifaniziro chake chosema. Wachiweramira ndi kuchigwadira n’kumapemphera pamaso pake kuti: “Ndipulumutseni, pakuti ndinu mulungu wanga.”+
41 Mitundu imeneyi inali kuopa Yehova,+ koma inali kutumikira zifaniziro zawo zogoba. Mpaka lero, ana awo ndi zidzukulu zawo akuchitabe mmene makolo awo ankachitira.
17 Koma mtengo wotsalawo wapangira mulungu, wapangira chifaniziro chake chosema. Wachiweramira ndi kuchigwadira n’kumapemphera pamaso pake kuti: “Ndipulumutseni, pakuti ndinu mulungu wanga.”+