1 Mafumu 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iye anali ndi akazi olemekezeka 700, ndi akazi ena apambali 300. M’kupita kwa nthawi,+ akazi amenewa anapotoza mtima wa Solomo. 1 Mafumu 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Palibenso munthu wina wofanana ndi Ahabu.+ Iye anadzipereka kuti achite zoipa pamaso pa Yehova ndiponso mkazi wake Yezebeli+ anamulimbikitsa+ kuchita zimenezo.
3 Choncho iye anali ndi akazi olemekezeka 700, ndi akazi ena apambali 300. M’kupita kwa nthawi,+ akazi amenewa anapotoza mtima wa Solomo.
25 Palibenso munthu wina wofanana ndi Ahabu.+ Iye anadzipereka kuti achite zoipa pamaso pa Yehova ndiponso mkazi wake Yezebeli+ anamulimbikitsa+ kuchita zimenezo.