2 Mafumu 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komabe Yehova sanabweze mkwiyo wake waukulu umene unayakira Yuda,+ chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene Manase anawachititsa, n’kukwiyitsa nazo Mulungu.+ 2 Mbiri 36:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye anapitiriza kuchita zoipa+ pamaso pa Yehova Mulungu wake, ndipo sanadzichepetse+ pamaso pa mneneri+ Yeremiya+ yemwe anapita kwa iye molamulidwa ndi Yehova. Danieli 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Inu Yehova, manyazi aphimba nkhope zathu, za mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu chifukwa takuchimwirani.+
26 Komabe Yehova sanabweze mkwiyo wake waukulu umene unayakira Yuda,+ chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene Manase anawachititsa, n’kukwiyitsa nazo Mulungu.+
12 Iye anapitiriza kuchita zoipa+ pamaso pa Yehova Mulungu wake, ndipo sanadzichepetse+ pamaso pa mneneri+ Yeremiya+ yemwe anapita kwa iye molamulidwa ndi Yehova.
8 “Inu Yehova, manyazi aphimba nkhope zathu, za mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu chifukwa takuchimwirani.+