Yeremiya 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Awa ndi mawu amene Yeremiya anauzidwa onena za anthu onse a mu Yuda m’chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, chimenenso chinali chaka choyamba cha ulamuliro wa Nebukadirezara mfumu ya Babulo. Yeremiya 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno m’chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, Yehova anauza Yeremiya kuti:
25 Awa ndi mawu amene Yeremiya anauzidwa onena za anthu onse a mu Yuda m’chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, chimenenso chinali chaka choyamba cha ulamuliro wa Nebukadirezara mfumu ya Babulo.
36 Ndiyeno m’chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu+ mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, Yehova anauza Yeremiya kuti: