Yeremiya 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Tsoka lidzamasulidwa kuchokera kumpoto ndipo lidzagwera anthu onse okhala m’dzikoli.+ Yeremiya 46:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Munthu waliwiro ndi munthu wamphamvu asayese dala kuthawa.+ Iwo apunthwa ndi kugwa.+ Zimenezi zachitikira kumpoto+ m’mphepete mwa mtsinje wa Firate.’
14 Pamenepo Yehova anandiuza kuti: “Tsoka lidzamasulidwa kuchokera kumpoto ndipo lidzagwera anthu onse okhala m’dzikoli.+
6 ‘Munthu waliwiro ndi munthu wamphamvu asayese dala kuthawa.+ Iwo apunthwa ndi kugwa.+ Zimenezi zachitikira kumpoto+ m’mphepete mwa mtsinje wa Firate.’