Ezekieli 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ukonze msewu woti lupanga lidzadutsemo pokaukira mzinda wa Raba+ wa ana a Amoni, ndi msewu wina woti lidzadutsemo pokaukira Yuda, inde pokaukira mzinda wa Yerusalemu wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri.+
20 Ukonze msewu woti lupanga lidzadutsemo pokaukira mzinda wa Raba+ wa ana a Amoni, ndi msewu wina woti lidzadutsemo pokaukira Yuda, inde pokaukira mzinda wa Yerusalemu wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri.+