Obadiya 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mtima wako wodzikuza wakunyenga,+ iwe amene ukukhala m’malo obisika a m’thanthwe+ pamwamba pa phiri. Iwe ukunena mumtima mwako kuti, ‘Ndani angandigwetsere pansi?’
3 Mtima wako wodzikuza wakunyenga,+ iwe amene ukukhala m’malo obisika a m’thanthwe+ pamwamba pa phiri. Iwe ukunena mumtima mwako kuti, ‘Ndani angandigwetsere pansi?’