2 Mbiri 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Panalinso anthu 10,000 amene ana a Yuda anawagwira amoyo. Choncho anapita nawo pathanthwe lomwe linali pamwamba kwambiri n’kuyamba kuwaponya kuchokera pathanthwepo ndipo onsewo anaphulikaphulika.+
12 Panalinso anthu 10,000 amene ana a Yuda anawagwira amoyo. Choncho anapita nawo pathanthwe lomwe linali pamwamba kwambiri n’kuyamba kuwaponya kuchokera pathanthwepo ndipo onsewo anaphulikaphulika.+