Obadiya 3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mtima wako wodzikuza wakunyenga,+ iwe amene ukukhala m’malo obisika a m’thanthwe+ pamwamba pa phiri. Iwe ukunena mumtima mwako kuti, ‘Ndani angandigwetsere pansi?’ Machitidwe 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 (Chotero munthu ameneyu, anagula+ munda ndi malipiro a ntchito zosalungama.+ Anagwa chamutu+ n’kuphulika mimba, moti phokoso la kuphulikako linamveka, ndipo matumbo ake onse anakhuthuka.
3 Mtima wako wodzikuza wakunyenga,+ iwe amene ukukhala m’malo obisika a m’thanthwe+ pamwamba pa phiri. Iwe ukunena mumtima mwako kuti, ‘Ndani angandigwetsere pansi?’
18 (Chotero munthu ameneyu, anagula+ munda ndi malipiro a ntchito zosalungama.+ Anagwa chamutu+ n’kuphulika mimba, moti phokoso la kuphulikako linamveka, ndipo matumbo ake onse anakhuthuka.