Yeremiya 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mikango yamphamvu imamubangulira.+ Imamutulutsira mawu awo.+ Ndipo yapangitsa dziko lake kukhala chinthu chodabwitsa kwa ena. Mizinda yake aiyatsa moto, choncho simukukhala munthu aliyense.+
15 Mikango yamphamvu imamubangulira.+ Imamutulutsira mawu awo.+ Ndipo yapangitsa dziko lake kukhala chinthu chodabwitsa kwa ena. Mizinda yake aiyatsa moto, choncho simukukhala munthu aliyense.+