Yesaya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa makamu akanapanda kutisiyira anthu ochepa opulumuka,+ tikanakhala ngati Sodomu, ndipo tikanafanana ndi Gomora.+ Mika 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzapondaponda zolakwa zathu.+ Machimo athu onse mudzawaponya pakati pa nyanja yozama.+
9 Yehova wa makamu akanapanda kutisiyira anthu ochepa opulumuka,+ tikanakhala ngati Sodomu, ndipo tikanafanana ndi Gomora.+
19 Inu mudzatichitiranso chifundo+ ndipo mudzapondaponda zolakwa zathu.+ Machimo athu onse mudzawaponya pakati pa nyanja yozama.+