Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 50:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova, m’dzikomo simudzakhalanso anthu+ ndipo dziko lonselo lidzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi Babulo adzayang’ana modabwa ndi kumuimbira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+

  • Yeremiya 51:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 “Taonani! Sesaki walandidwa.+ Dziko lotamandidwa padziko lonse lapansi latengedwa.+ Babulo wakhala chinthu chodabwitsa pakati pa mitundu ya anthu.+

  • Chivumbulutso 18:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 ndipo azidzati, ‘Kalanga ine! Kalanga ine! Mzinda waukuluwe+ wovala zovala zapamwamba, zofiirira, ndi zofiira kwambiri. Mzinda wokongoletsedwa mochititsa kaso iwe, ndi zokongoletsera zagolide, zamwala wamtengo wapatali, ndi zangale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena