Mateyu 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zilekeni zonse zikulire pamodzi mpaka nthawi yokolola. M’nyengo yokolola ndidzauza okololawo kuti, Choyamba sonkhanitsani namsongole ndi kumumanga m’mitolo kuti akatenthedwe.+ Mukatha mupite kukasonkhanitsa tirigu ndi kumuika m’nkhokwe yanga.’”+ Chivumbulutso 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mngelo wina anatuluka m’nyumba yopatulika ya pakachisi, akufuula kwa wokhala pamtambo uja ndi mawu okweza, kuti: “Tsitsa chikwakwa chako ndi kuyamba kumweta,+ chifukwa ola la kumweta lafika.+ Pakuti zokolola za padziko lapansi zapsa bwino.”+
30 Zilekeni zonse zikulire pamodzi mpaka nthawi yokolola. M’nyengo yokolola ndidzauza okololawo kuti, Choyamba sonkhanitsani namsongole ndi kumumanga m’mitolo kuti akatenthedwe.+ Mukatha mupite kukasonkhanitsa tirigu ndi kumuika m’nkhokwe yanga.’”+
15 Mngelo wina anatuluka m’nyumba yopatulika ya pakachisi, akufuula kwa wokhala pamtambo uja ndi mawu okweza, kuti: “Tsitsa chikwakwa chako ndi kuyamba kumweta,+ chifukwa ola la kumweta lafika.+ Pakuti zokolola za padziko lapansi zapsa bwino.”+