1 Mafumu 7:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Anapanganso zoikapo nyale+ zagolide woyenga bwino,+ n’kukaziika pafupi ndi chipinda chamkati, zisanu mbali ya kudzanja lamanja, zisanu mbali ya kumanzere. Ndiponso anapanga maluwa+ agolide, nyale+ zagolide, zopanira+ zagolide zozimitsira nyale,
49 Anapanganso zoikapo nyale+ zagolide woyenga bwino,+ n’kukaziika pafupi ndi chipinda chamkati, zisanu mbali ya kudzanja lamanja, zisanu mbali ya kumanzere. Ndiponso anapanga maluwa+ agolide, nyale+ zagolide, zopanira+ zagolide zozimitsira nyale,