Deuteronomo 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mungathe kuwononga mtengo wokhawo umene mukuudziwa kuti subereka zipatso zakudya. Mtengo woterowo mungaudule ndi kumangira mpanda wozungulira+ mzinda wa adani umene ukuchita nanu nkhondo, kufikira mzindawo utagwa.
20 Mungathe kuwononga mtengo wokhawo umene mukuudziwa kuti subereka zipatso zakudya. Mtengo woterowo mungaudule ndi kumangira mpanda wozungulira+ mzinda wa adani umene ukuchita nanu nkhondo, kufikira mzindawo utagwa.