Yeremiya 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atatero, Yeremiya anauza akalonga onse ndi anthu onse kuti: “Yehova ndi amene anandituma kuti ndidzanenere mawu onse amene mwamva okhudza nyumba iyi ndi mzinda uwu.+ Danieli 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Sitinamvere atumiki anu aneneri,+ amene analankhula m’dzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu, ndi anthu onse a m’dziko lathu.+
12 Atatero, Yeremiya anauza akalonga onse ndi anthu onse kuti: “Yehova ndi amene anandituma kuti ndidzanenere mawu onse amene mwamva okhudza nyumba iyi ndi mzinda uwu.+
6 Sitinamvere atumiki anu aneneri,+ amene analankhula m’dzina lanu kwa mafumu athu, akalonga athu, makolo athu, ndi anthu onse a m’dziko lathu.+