Mateyu 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anawauza kuti: “Malemba amati, ‘Nyumba yanga idzatchedwa nyumba yopemphereramo,’+ koma inu mukuisandutsa phanga la achifwamba.”+ Maliko 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno anayamba kuphunzitsa ndi kunena kuti: “Kodi Malemba sanena kuti, ‘Nyumba yanga idzatchedwa nyumba yopemphereramo+ mitundu yonse’?+ Koma inu mwaisandutsa phanga la achifwamba.”+ Luka 19:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 ndi kuwauza kuti: “Malemba amati, ‘Nyumba yanga idzakhala nyumba yopemphereramo,’+ koma inu mwaisandutsa phanga la achifwamba.”+
13 Iye anawauza kuti: “Malemba amati, ‘Nyumba yanga idzatchedwa nyumba yopemphereramo,’+ koma inu mukuisandutsa phanga la achifwamba.”+
17 Ndiyeno anayamba kuphunzitsa ndi kunena kuti: “Kodi Malemba sanena kuti, ‘Nyumba yanga idzatchedwa nyumba yopemphereramo+ mitundu yonse’?+ Koma inu mwaisandutsa phanga la achifwamba.”+
46 ndi kuwauza kuti: “Malemba amati, ‘Nyumba yanga idzakhala nyumba yopemphereramo,’+ koma inu mwaisandutsa phanga la achifwamba.”+