Yeremiya 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi nyumba iyi, imene yatchedwa ndi dzina langa,+ mwayamba kuiona ngati phanga la achifwamba?+ Inetu ndaona zimene mukuchita,” watero Yehova.+ Maliko 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno anayamba kuphunzitsa ndi kunena kuti: “Kodi Malemba sanena kuti, ‘Nyumba yanga idzatchedwa nyumba yopemphereramo+ mitundu yonse’?+ Koma inu mwaisandutsa phanga la achifwamba.”+ Luka 19:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 ndi kuwauza kuti: “Malemba amati, ‘Nyumba yanga idzakhala nyumba yopemphereramo,’+ koma inu mwaisandutsa phanga la achifwamba.”+ Yohane 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano anauza ogulitsa nkhundawo kuti: “Chotsani izi muno! Mulekeretu kusandutsa nyumba+ ya Atate wanga kukhala nyumba ya malonda!”+
11 Kodi nyumba iyi, imene yatchedwa ndi dzina langa,+ mwayamba kuiona ngati phanga la achifwamba?+ Inetu ndaona zimene mukuchita,” watero Yehova.+
17 Ndiyeno anayamba kuphunzitsa ndi kunena kuti: “Kodi Malemba sanena kuti, ‘Nyumba yanga idzatchedwa nyumba yopemphereramo+ mitundu yonse’?+ Koma inu mwaisandutsa phanga la achifwamba.”+
46 ndi kuwauza kuti: “Malemba amati, ‘Nyumba yanga idzakhala nyumba yopemphereramo,’+ koma inu mwaisandutsa phanga la achifwamba.”+
16 Tsopano anauza ogulitsa nkhundawo kuti: “Chotsani izi muno! Mulekeretu kusandutsa nyumba+ ya Atate wanga kukhala nyumba ya malonda!”+