1 Samueli 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Poyankha Samueli anati: “Kodi Yehova amakondwera ndi nsembe zopsereza+ ndi nsembe zina kuposa kumvera mawu a Yehova? Taona! Kumvera+ kuposa nsembe,+ ndipo kumvetsera mosamala kuposa mafuta+ a nkhosa zamphongo. Salimo 51:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti nsembe singakusangalatseni, chifukwa ikanakusangalatsani ndikanaipereka kwa inu.+Nsembe yopsereza yathunthu singakusangalatseni.+ Hoseya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndimakondwera ndi kukoma mtima kosatha,+ osati ndi nsembe.+ Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati ndi nsembe zopsereza zathunthu.+
22 Poyankha Samueli anati: “Kodi Yehova amakondwera ndi nsembe zopsereza+ ndi nsembe zina kuposa kumvera mawu a Yehova? Taona! Kumvera+ kuposa nsembe,+ ndipo kumvetsera mosamala kuposa mafuta+ a nkhosa zamphongo.
16 Pakuti nsembe singakusangalatseni, chifukwa ikanakusangalatsani ndikanaipereka kwa inu.+Nsembe yopsereza yathunthu singakusangalatseni.+
6 Pakuti ndimakondwera ndi kukoma mtima kosatha,+ osati ndi nsembe.+ Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati ndi nsembe zopsereza zathunthu.+