Yeremiya 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Yehova wanena kuti: “Chotero taonani! Masiku akubwera pamene sadzatchulanso malowo kuti Tofeti+ ndiponso chigwa cha mwana wa Hinomu,+ koma adzawatchula kuti chigwa chopherako anthu.
6 “‘Yehova wanena kuti: “Chotero taonani! Masiku akubwera pamene sadzatchulanso malowo kuti Tofeti+ ndiponso chigwa cha mwana wa Hinomu,+ koma adzawatchula kuti chigwa chopherako anthu.