Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 23:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mfumuyo inachititsa kuti ku Tofeti,+ m’chigwa cha ana a Hinomu+ kukhale kosayenera kulambirako, kuti munthu aliyense asawotcheko* mwana wake wamwamuna kapena mwana wake wamkazi pamoto,+ pomupereka kwa Moleki.+

  • Yesaya 30:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Malo otchedwa Tofeti*+ owonongerako Asuri akonzedwa kale. Malowo akonzedweranso mfumu yawo.+ Malo amene iye wakonzawo ndi ozama ndipo kuli moto waukulu ndi nkhuni zambiri. Mpweya wa Yehova ukuyatsa malowo ngati mtsinje wa sulufule.+

  • Yeremiya 7:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 “‘Chotero taonani! Masiku akubwera,’ watero Yehova, ‘pamene sadzatchulanso malowo kuti Tofeti ndiponso chigwa cha mwana wa Hinomu, koma adzawatchula kuti chigwa chopherako anthu.+ Iwo adzaika anthu m’manda ku Tofeti mpaka sikudzakhala malo okwanira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena