Yesaya 37:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pamene Senakeribu anali kugwada m’kachisi wa mulungu wake+ Nisiroki,+ ana ake Adarameleki ndi Sarezere anamupha ndi lupanga,+ iwo n’kuthawira kudziko la Ararati.+ Kenako Esari-hadoni+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. Ezekieli 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kumeneko n’kumene kuli Asuri ndi khamu lake lonse.+ Manda a anthu a ku Asuri ali mozungulira mfumu yawo. Onsewo anaphedwa ndi lupanga.+
38 Pamene Senakeribu anali kugwada m’kachisi wa mulungu wake+ Nisiroki,+ ana ake Adarameleki ndi Sarezere anamupha ndi lupanga,+ iwo n’kuthawira kudziko la Ararati.+ Kenako Esari-hadoni+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
22 Kumeneko n’kumene kuli Asuri ndi khamu lake lonse.+ Manda a anthu a ku Asuri ali mozungulira mfumu yawo. Onsewo anaphedwa ndi lupanga.+