Yesaya 37:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno mngelo+ wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri n’kukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka m’mawa, anangoona kuti onse aja ndi mitembo yokhayokha.+ Zekariya 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzadutsa panyanja, nyanjayo nditaigwetsera tsoka.+ Ndidzamenya mafunde a nyanjayo+ ndipo madzi onse a mtsinje wa Nailo adzauma.+ Kunyada kwa Asuri kudzathetsedwa+ ndipo ndodo yachifumu+ ya Iguputo idzachoka.+
36 Ndiyeno mngelo+ wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri n’kukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka m’mawa, anangoona kuti onse aja ndi mitembo yokhayokha.+
11 Ndidzadutsa panyanja, nyanjayo nditaigwetsera tsoka.+ Ndidzamenya mafunde a nyanjayo+ ndipo madzi onse a mtsinje wa Nailo adzauma.+ Kunyada kwa Asuri kudzathetsedwa+ ndipo ndodo yachifumu+ ya Iguputo idzachoka.+