Ezekieli 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Asuri ali kumeneko limodzi ndi gulu lake lonse. Manda a anthu a ku Asuri ali mozungulira mfumu yawo. Onsewo anaphedwa ndi lupanga.+
22 Asuri ali kumeneko limodzi ndi gulu lake lonse. Manda a anthu a ku Asuri ali mozungulira mfumu yawo. Onsewo anaphedwa ndi lupanga.+