Ezekieli 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kumeneko n’kumene kuli Asuri ndi khamu lake lonse.+ Manda a anthu a ku Asuri ali mozungulira mfumu yawo. Onsewo anaphedwa ndi lupanga.+
22 Kumeneko n’kumene kuli Asuri ndi khamu lake lonse.+ Manda a anthu a ku Asuri ali mozungulira mfumu yawo. Onsewo anaphedwa ndi lupanga.+