Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Udzalonjeza kukwatira mkazi koma mwamuna wina adzamugwirira.+ Udzamanga nyumba koma sudzakhalamo.+ Udzabzala mitengo ya mpesa koma sudzadya zipatso zake.+

  • Yeremiya 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Nyumba zawo, minda yawo ndi akazi awo, zonse pamodzi zidzaperekedwa kwa anthu ena.+ Pakuti ine ndidzatambasula dzanja langa ndi kuwononga anthu okhala m’dzikoli,” watero Yehova.+

  • Amosi 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Inu mukulamula anthu osauka kuti akulipireni mwa kukupatsani zokolola zawo za m’munda, ndiponso kuti azikhoma msonkho mwa kupereka mbewu za m’munda.+ Choncho chifukwa mwachita zinthu zimenezi, simudzapitiriza kukhala m’nyumba zamiyala yosema zimene mwamanga+ ndipo simudzamwa vinyo wochokera m’minda yanu ya mpesa yosiririkayo.+

  • Zefaniya 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chuma chawo chidzafunkhidwa ndipo nyumba zawo zidzakhala bwinja.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.+ Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wochokera mmenemo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena