Yeremiya 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho mvula yamvumbi yasiya kugwa,+ ndipo mvula yomalizira siinagwe.+ Ukuchita zinthu mopanda manyazi ngati mkazi amene akuchita uhule.* Palibe chimene chikukuchititsa manyazi.+ Afilipi 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amenewo mapeto awo ndi chiwonongeko,+ ndipo mulungu wawo ndi mimba yawo.+ Ulemerero wawo uli m’zinthu zawo zochititsa manyazi,+ ndipo maganizo awo ali pa zinthu za dziko lapansi.+
3 Choncho mvula yamvumbi yasiya kugwa,+ ndipo mvula yomalizira siinagwe.+ Ukuchita zinthu mopanda manyazi ngati mkazi amene akuchita uhule.* Palibe chimene chikukuchititsa manyazi.+
19 Amenewo mapeto awo ndi chiwonongeko,+ ndipo mulungu wawo ndi mimba yawo.+ Ulemerero wawo uli m’zinthu zawo zochititsa manyazi,+ ndipo maganizo awo ali pa zinthu za dziko lapansi.+