Yeremiya 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Abale ako komanso anthu a m’nyumba ya bambo ako akuchitira chinyengo,+ ndipo mofuula akukunenera zinthu zoipa ali kumbuyo kwako. Usawakhulupirire m’pang’ono pomwe, ngakhale kuti akukuuza mawu abwino.+ Mika 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu okhulupirika atha padziko lapansi, ndipo pakati pa anthu palibe munthu wowongoka mtima.+ Onse amadikirira anzawo kuti akhetse magazi.+ Aliyense amasaka m’bale wake ndi ukonde.+
6 Abale ako komanso anthu a m’nyumba ya bambo ako akuchitira chinyengo,+ ndipo mofuula akukunenera zinthu zoipa ali kumbuyo kwako. Usawakhulupirire m’pang’ono pomwe, ngakhale kuti akukuuza mawu abwino.+
2 Anthu okhulupirika atha padziko lapansi, ndipo pakati pa anthu palibe munthu wowongoka mtima.+ Onse amadikirira anzawo kuti akhetse magazi.+ Aliyense amasaka m’bale wake ndi ukonde.+