Ezekieli 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Nditati ndichititse zilombo zolusa zakutchire kudutsa m’dzikolo,+ zilombozo n’kuliphera ana dzikolo,+ moti dzikolo n’kukhala bwinja lokhalokha popanda munthu aliyense wodutsamo chifukwa cha zilombo zolusazo,+
15 “‘Nditati ndichititse zilombo zolusa zakutchire kudutsa m’dzikolo,+ zilombozo n’kuliphera ana dzikolo,+ moti dzikolo n’kukhala bwinja lokhalokha popanda munthu aliyense wodutsamo chifukwa cha zilombo zolusazo,+