Levitiko 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzatumiza zilombo zakutchire pakati panu,+ ndipo zidzakupherani ana anu+ ndi ziweto zanu, ndi kuchepetsa chiwerengero chanu, moti m’misewu yanu mudzakhala mopanda anthu.+ 2 Mafumu 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pomalizira pake Elisa anatembenuka ndipo anawaona. Atatero anawaitanira tsoka+ m’dzina la Yehova. Kenako zimbalangondo ziwiri zazikazi+ zinatuluka m’thengo n’kukhadzulapo anyamata 42.+
22 Ndidzatumiza zilombo zakutchire pakati panu,+ ndipo zidzakupherani ana anu+ ndi ziweto zanu, ndi kuchepetsa chiwerengero chanu, moti m’misewu yanu mudzakhala mopanda anthu.+
24 Pomalizira pake Elisa anatembenuka ndipo anawaona. Atatero anawaitanira tsoka+ m’dzina la Yehova. Kenako zimbalangondo ziwiri zazikazi+ zinatuluka m’thengo n’kukhadzulapo anyamata 42.+