Yesaya 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mimbulu izidzalira munsanja zake zokhalamo,+ ndipo njoka zikuluzikulu zizidzakhala m’nyumba zachifumu zokongola. Nyengo yake yatsala pang’ono kufika, ndipo masiku ake sadzatalikitsidwa.”+ Yeremiya 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tamvetserani nkhani imene yamveka! Kugunda kwakukulu kukumveka kuchokera kudziko la kumpoto,+ ndipo kudzasandutsa mizinda ya Yuda kukhala mabwinja, malo obisalamo mimbulu.+
22 Mimbulu izidzalira munsanja zake zokhalamo,+ ndipo njoka zikuluzikulu zizidzakhala m’nyumba zachifumu zokongola. Nyengo yake yatsala pang’ono kufika, ndipo masiku ake sadzatalikitsidwa.”+
22 Tamvetserani nkhani imene yamveka! Kugunda kwakukulu kukumveka kuchokera kudziko la kumpoto,+ ndipo kudzasandutsa mizinda ya Yuda kukhala mabwinja, malo obisalamo mimbulu.+