Yeremiya 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova wanena kuti: “Dziko lonseli lidzakhala bwinja+ ndipo ndidzawafafaniza.+ Yeremiya 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dziko lonseli lidzakhala bwinja, chinthu chodabwitsa, ndipo mitundu imeneyi idzatumikira mfumu ya ku Babulo zaka 70.”’+ Yeremiya 32:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Anthu adzagula minda m’dziko lino,+ dziko limene anthu inu mudzanena kuti: “Dziko ili ndi bwinja,+ lopanda munthu wokhalamo kapena nyama yoweta. Linaperekedwa m’manja mwa Akasidi.”’+
11 Dziko lonseli lidzakhala bwinja, chinthu chodabwitsa, ndipo mitundu imeneyi idzatumikira mfumu ya ku Babulo zaka 70.”’+
43 Anthu adzagula minda m’dziko lino,+ dziko limene anthu inu mudzanena kuti: “Dziko ili ndi bwinja,+ lopanda munthu wokhalamo kapena nyama yoweta. Linaperekedwa m’manja mwa Akasidi.”’+